Skip to content Skip to sidebar Skip to footer

(Download) "KODI MWABADWADI MWATSOPANO MWA MADZI NDI MZIMU?" by Paul C. Jong # eBook PDF Kindle ePub Free

KODI MWABADWADI MWATSOPANO MWA MADZI NDI MZIMU?

📘 Read Now     📥 Download


eBook details

  • Title: KODI MWABADWADI MWATSOPANO MWA MADZI NDI MZIMU?
  • Author : Paul C. Jong
  • Release Date : January 05, 2021
  • Genre: Christianity,Books,Religion & Spirituality,
  • Pages : * pages
  • Size : 1953 KB

Description

Ndime yamuthu waukhulu ya m'nkhaniyi ndi "ku Badwanso mwa Madzi ndi Mzimu." Muthuyu wachoka mnkhani yomweyi. Kunenetsa, bukuli likufothokoza tanthauzo lakubadwanso ndi mwamene mungabadwirenso mwa madzi ndi Mzimu mogwirizana ndi Bibulo. Madzi akuimirira ubadizo wa Yesu mu Yordani ndipo Babilo likuti machismo athu tonse anaikidwa pa Yesuyo pamene anabadizidwa ndi Yohane Mbatizi. Yohane ankhaimilira anthu amitundu yosina-siyana anali wambanja la Aloni wa Sembe Wamkhulu. Aloniyo aikha manja ake pa mbuzi yopepetsera machimo a Asiraeli achaka chonse Patsiku la Kupepetsera Machismo. Chinali chinthunzi-thunzi cha zinthu zabwino zikubwera. Kubadizidwa kwa Yesu kukufanizira kuikhapo manja kuja. Yesu anabadizidwa m'njira yoikha manja ku mtsinje wa Yordani uja. Ndiye anachotsa machismo adziko lonse paubadizo Wake ndipo anapachikidwa kuti alipe machimo athu. Koma anthu ambiri sakudziwa nchifukwa chanji Yesu anabadizidwa ndi Yohani mu Yordani. Ubadizo wa Yesu ndiyo nfundo yaikhulu mbukuli, imene singasiyanitsidwe ndi Uthenga wa Bwino wa madzi ndi Mzimu. Tingabadwenso ngati tikhulupirira mu ubadizo wa Yesu ndi Mtanda Wake.


PDF Books Download "KODI MWABADWADI MWATSOPANO MWA MADZI NDI MZIMU?" Online ePub Kindle